Ezekieli 37:24 BL92

24 Ndi mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yao, ndipo iwo onse adzakhala ndi mbusa mmodzi, adzayendanso m'maweruzo anga, nadzasunga malemba anga ndi kuwacita.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:24 nkhani