6 Pamenepo anafika ku cipata coloza kum'mawa, nakwera pa makwerero ace; ndipo anayesa ciundo ca cipata, bango limodzi kucindikira kwace; ndico ciundo coyamba, bango limodzi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40
Onani Ezekieli 40:6 nkhani