Ezekieli 9:7 BL92

7 Nati kwa iwo, Muipse nyumbayi ndi kudzaza mabwalo ndi ophedwa, mukani. Ndipo anaturuka, nakantha m'mudzimo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 9

Onani Ezekieli 9:7 nkhani