Yeremiya 10:16 BL92

16 Gawo la Yakobo silifanana ndi iwo; pakuti iye ndiye analenga zonse; Israyeli ndiye mtundu wa colowa cace; dzina lace ndi Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10

Onani Yeremiya 10:16 nkhani