20 Hema wanga waonongeka, zingwe zanga zonse zaduka; ana anga aturuka mwa ine, palibe iwo; palibenso amene adzamanga hema wanga, kapena kucinga nsaru zanga,
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10
Onani Yeremiya 10:20 nkhani