Yeremiya 11:12 BL92

12 Ndipo midzi ya Yuda ndi okhala m'Yerusalemu adzapita nadzapfuulira kwa milungu imene anaifukizira; koma siidzawapulumutsa konse nthawi ya nsautso yao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11

Onani Yeremiya 11:12 nkhani