20 Koma, Yehova wa makamu, amene aweruza molungama, pamene ayesa imso ndi mtima, ndikuoneni Inu mulikuwabwezera cilango, pakuti kwa Inu ndaulula mlandu wanga.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11
Onani Yeremiya 11:20 nkhani