Yeremiya 12:6 BL92

6 Pakuti ngakhale abale ako, ndi nyumba ya atate wako, ngakhale iwo anakunyenga iwe; ngakhale anakupfuulira iwe; usamvere iwo, ngakhale anena nawe mau abwino.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 12

Onani Yeremiya 12:6 nkhani