Yeremiya 14:10 BL92

10 Atero Yehova kwa anthu awa, Comwecoakonda kusocerera; sanakaniza mapazi ao; cifukwa cace. Yehova sawalandira; tsopano adzakumbukira coipa cao, nadzalanga zocimwa zao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:10 nkhani