Yeremiya 14:12 BL92

12 Pamene asala cakudya, sindidzamva kupfuula kwao; ndipo pamene apereka nsembe yopsereza, ndi nsembe yaufa sindidzawalandira; koma ndidzawatha ndi lupanga, ndi cirala, ndi caola.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:12 nkhani