Yeremiya 14:15 BL92

15 Cifukwa cace atero Yehova za aneneri onenera m'dzina langa, ndipo sindinawatuma, koma ati, Lupanga ndi cirala sizidzakhala m'dziko muno; ndi lupanga ndi cirala aneneriwo adzathedwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:15 nkhani