Yeremiya 14:17 BL92

17 Ndipo udzati kwa iwo mau awa, Maso anga agwe misozi usana ndi usiku, asaleke; pakuti namwali mwana wa anthu anga wasweka ndi kusweka kwakukuru, ndi bala lopweteka kwambiri.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:17 nkhani