Yeremiya 15:20 BL92

20 Ndidzakuyesa iwe linga lamkuwa la anthu awa; ndipe adzamenyana ndi iwe, koma iwo sadzakuposa iwe; pakuti Ine ndiri ndi iwe kuti ndikupulumutse ndi kukulanditsa iwe, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 15

Onani Yeremiya 15:20 nkhani