Yeremiya 16:21 BL92

21 Cifukwa cace, taonani, ndidzadziwitsa iwo kamodzi aka, ndidzawadziwitsa dzanja langa ndi mphamvu yanga; ndipo adzadziwa kuti dzina langa ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16

Onani Yeremiya 16:21 nkhani