9 Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli; Taonani, ndidzaletsa pano, pamaso panu masiku anu, mau akukondwerera ndi mau akusangalala, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16
Onani Yeremiya 16:9 nkhani