Yeremiya 17:11 BL92

11 Monga nkhwali iumatira pa mazira amene sinaikira, momwemo iye amene asonkhanitsa cuma, koma mosalungama; pakati pa masiku ace cidzamsiya iye, ndipo pa citsirizo adzakhala wopusa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:11 nkhani