Yeremiya 17:14 BL92

14 Mundiciritse ine, Yehova, ndipo ndidzaciritsidwa; mundipulumutse ine, ndipo ndidzapulumutsidwa; pakuti cilemekezo canga ndinu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:14 nkhani