16 Koma ine, pokhala mbusa sindinafulumira kucokerako kuti ndikutsateni Inu; sindinakhumba tsiku la tsoka; Inu mudziwa, cimene cinaturuka pa milomo yanga cinali pamaso panu.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17
Onani Yeremiya 17:16 nkhani