Yeremiya 17:24 BL92

24 Ndipo padzakhala, ngati mu ndimveretsa Ine, ati Yehova, kuti musalowetse katundu pa zipata za mudzi uwu tsiku la Sabata, koma mupatule tsiku la Sabata, osagwira nchito m'menemo;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:24 nkhani