Yeremiya 18:22 BL92

22 Mpfuu umvekedwe m'nyumba zao, pamene muwatengera khamu la nkhondo dzidzidzi; pakuti akumba dzenje lakundigwira ine, anabisira mapazi anga misampha.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 18

Onani Yeremiya 18:22 nkhani