10 Pakuti pitani ku zisumbu za Kitimu nimuone; tumizani ku Kedara nimulingalire bwino; nimuone ngati cinalipo cotere.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2
Onani Yeremiya 2:10 nkhani