Yeremiya 2:26 BL92

26 Monga mbala iri ndi manyazi pamene igwidwa, comweco nyumba ya Israyeli iri ndi manyazi; iwo, mafumu ao, akuru ao, ansembe ao, ndi aneneri ao;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2

Onani Yeremiya 2:26 nkhani