31 Mbadwo inu, taonani mau a Yehova. Kodi ndakhala kwa Israyeli cipululu? Kapena dziko la mdima woti bii? Cifukwa ninji ati anthu anga, Tamasuka sitidzabweranso konse kwa Inu?
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2
Onani Yeremiya 2:31 nkhani