7 Ndipo ndinakulowetsani m'dziko la minda, kuti mudye zipatso zace, ndi zabwino zace; koma pamene munalowa, munaipitsa dziko langa, ndi kuyesa colandira canga conyansa.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2
Onani Yeremiya 2:7 nkhani