1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wace wa Maseya wansembe, akati,
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 21
Onani Yeremiya 21:1 nkhani