Yeremiya 21:13 BL92

13 Taonani, Ine ndine mdani wako, iwe wokhala m'cigwa, ndi pa thanthwe la m'cidikha, ati Yehova; inu amene muti, Ndani adzatsikira kumenyana ndi ife? ndani adzalowa m'zokhalamo zathu?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 21

Onani Yeremiya 21:13 nkhani