10 Musamlirire wakufa, musacite maliro ace; koma mumliritse iye amene amuka, pakuti sadzabweranso, kapena kuonanso dziko la kwao.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22
Onani Yeremiya 22:10 nkhani