Yeremiya 22:17 BL92

17 Koma maso ako ndi mtima wako sizisamalira kanthu koma kusirira, ndi kukhetsa mwazi wosacimwa, ndi kusautsa, ndi zaciwawa, kuti uzicite.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22

Onani Yeremiya 22:17 nkhani