Yeremiya 23:10 BL92

10 Pakuti dziko ladzala ndi acigololo; pakuti cifukwa ca temberero dziko lilira, mabusa a kucipululu auma; kuyenda kwao kuli koipa, ndi mphamvu yao siiri yabwino.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:10 nkhani