Yeremiya 23:28 BL92

28 Mneneri wokhala ndi loto, anene loto lace; ndi iye amene ali ndi mau anga, anene mau anga mokhulupirika. Kodi phesi ndi ciani polinganiza ndi tirigu? ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:28 nkhani