Yeremiya 23:33 BL92

33 Ndipo pamene anthu awa, kapena mneneri, kapena wansembe, adzakufunsa iwe, kuti, Katundu wa Yehova ndi ciani? pamenepo uziti kwa iwo, Katundu wanji? Ndidzakucotsani inu, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:33 nkhani