Yeremiya 23:39 BL92

39 cifukwa cace, taonani, ndidzakuiwalani inu konse, ndipo ndidzakucotsani, ndi mudzi umene ndinakupatsani inu ndi makolo anu, ndidzaucotsa pamaso panga;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:39 nkhani