Yeremiya 24:2 BL92

2 Mtanga umodzi unali ndi nkhuyu zabwinobwino, ngati nkhuyu zoyamba kuca; ndipo mtanga umodzi unali ndi nkhuyu zoipaipa, zosadyeka, zinali zoipa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 24

Onani Yeremiya 24:2 nkhani