9 Ndipo ndidzawapatsa akhale coopsetsa coipa ku maufumu a dziko lapansi; akhale citonzo ndi nkhani ndi coseketsa, ndi citemberero, monse m'mene ndidzawapitikitsiramo.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 24
Onani Yeremiya 24:9 nkhani