Yeremiya 25:38 BL92

38 Wasiya ngaka yace, monga mkango; pakuti dziko lao lasanduka cizizwitso cifukwa ca ukali wa lupanga losautsa, ndi cifukwa ca mkwiyo wace waukali.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:38 nkhani