Yeremiya 26:4 BL92

4 Ndipo iwe uziti kwa iwo, Yehova atero: Ngati simudzandimvera Ine kuyenda m'cilamulo canga, cimene ndaciika pamaso panu,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 26

Onani Yeremiya 26:4 nkhani