Yeremiya 27:1 BL92

1 Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 27

Onani Yeremiya 27:1 nkhani