11 Pakuti ndidziwa malingiriro amene ndilingiririra inu, ati Yehova, malingiriro a mtendere, si a coipa, akukupatsani inu adzukulu ndi ciyembekezero.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29
Onani Yeremiya 29:11 nkhani