Yeremiya 29:23 BL92

23 cifukwa anacita zopusa m'Israyeli, nacita cigololo ndi akazi a anansi ao, nanena mau onama m'dzina langa, amene ndinawauza kuti asanene; Ine ndine wodziwa, ndi mboni, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:23 nkhani