8 Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero: Aneneri anu ndi akuombeza anu amene akhala pakati panu, asakunyengeni inu, musamvere maloto anu amene mulotetsa.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29
Onani Yeremiya 29:8 nkhani