Yeremiya 3:5 BL92

5 Kodi adzasunga mkwiyo wace ku nthawi zonse? Kodi adzakudikira mpaka cimariziro? Taona, wanena ndi kucita zoipa monga unatero.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:5 nkhani