Yeremiya 30:14 BL92

14 Mabwenzi ako onse anakuiwala iwe; salikukufuna iwe; pakuti ndakulasa ndi bala la mdani, ndi kulanga kwa wankhanza; cifukwa ca mphulupulu yako yaikuru, cifukwa zocimwa zako zinacuruka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:14 nkhani