Yeremiya 30:24 BL92

24 Mkwiyo waukali wa Yehova sudzabwerera, mpaka wacita, mpaka watha zomwe afuna kucita m'mtima mwace: masiku akumariza mudzacizindikira.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:24 nkhani