Yeremiya 30:8 BL92

8 Pakuti padzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova wa makamu, kuti ndidzatyola gori lace pakhosi pako, ndipo ndidzadula zomangira zako; ndipo alendo sadzamuyesanso iye mtumiki wao;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:8 nkhani