Yeremiya 31:15 BL92

15 Atero Yehova: Mau amveka m'Rama, maliro ndi kulira kwakuwawa, Rakeli alinkulirira ana ace; akana kutonthozedwa mtima pa ana ace, cifukwa palibe iwo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:15 nkhani