Yeremiya 31:30 BL92

30 Koma yense adzafa cifukwa ca mphulupulu yace; yense amene adya mphesa zowawa, mano ace adzayayamira.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:30 nkhani