Yeremiya 31:32 BL92

32 si monga pangano limene ndinapangana ndi makolo ao tsiku lija ndinawagwira manja kuwaturutsa m'dziko la Aigupto; pangano langa limenelo analiswa, ngakhale ndinali mbuyao, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:32 nkhani