Yeremiya 31:36 BL92

36 Ngati malembawa acoka pamaso panga, ati Yehova, pamenepo mbeunso ya Israyeli idzaleka kukhala mtundu pamaso panga ku nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:36 nkhani