15 Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero: Nyumba ndi minda ndi minda yamphesa idzagulidwanso m'dziko muno.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:15 nkhani