18 a amene mucitira cifundo anthu zikwi; nimubwezera mphulupulu ya atate m'cifuwa ca ana ao a pambuyo pao, dzina lace ndi Mulungu wamkuru, wamphamvu, Yehova wa makamu;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:18 nkhani